Owner of MAIDEN INVESTMENTS🙌🏾
Abale, ma tarpaulin odula chonchi ndi a mtundu wanji? Ma tarpaulin akulu kwambiri a 60ft x 40ft ali pa K5.6 miliyoni kuphatikizapo VAT., 750gsm thickness yake. Pa ma tarpaulin 100 siikanadutsa K560 miliyoni. Ndiye mpaka K3 biliyoni mmmm, kuba kopanda nako manyazi.